Kalata kwa Dr. Joyce Banda

(Copied) Wokondeka Mayi Joyce Banda, Ndamvetsedwa kuti muli ku London kumene adakuyitanani a BBC kuti mukalankhule ndi azimayi amzanu. Zosangalatsa tu zimenezo mayi. Zimenezi zangotiwonetsera a Malaw...